10 Choncho ndinapita pamene iye anali ndi kumupha,+ chifukwa ndinadziwa kuti sakhalanso ndi moyo popeza anali atavulala kwambiri. Kenako ndinatenga chisoti chachifumu+ chimene anavala ndi khoza limene linali kudzanja lake kuti ndibwere nazo kuno kwa inu mbuyanga.”