Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 16:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Uzitsatira chilungamo.+ Ndithudi uzitsatira chilungamo kuti ukhale ndi moyo ndi kukatengadi dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa.+

  • Yobu 21:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Popeza mukuti, ‘Kodi nyumba ya wolemekezeka ili kuti,

      Ndipo hema wa oipa ali kuti? Kodi malo awo okhala ali kuti?’+

  • Salimo 37:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Patsala kanthawi kochepa, woipa sadzakhalakonso.+

      Udzayang’ana pamene anali kukhala, ndipo sadzapezekapo.+

  • Salimo 91:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Udzayang’ana ndi maso ako,+

      Ndipo udzaona anthu oipa akulandira chilango.+

  • Salimo 101:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 M’mawa uliwonse ndidzawononga oipa onse a padziko lapansi.+

      Ndidzapha ndi kuchotsa mumzinda wa Yehova anthu onse ochita zinthu zopweteka anzawo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena