Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 18:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “‘Usavule mlongo wako, mwana wamkazi wa bambo ako kapena mwana wamkazi wa mayi ako, kaya wobadwa naye m’banja limodzi kapena wobadwira m’banja lina, usawavule.+

  • Deuteronomo 27:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 “‘Wotembereredwa ndi munthu wogona ndi mlongo wake, mwana wamkazi wa bambo ake kapena mwana wamkazi wa mayi ake.’+ (Anthu onse ayankhe kuti, ‘Zikhale momwemo!’)

  • 2 Samueli 13:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Koma Tamara anamuuza kuti: “Ayi, m’bale wanga! Usandichititse manyazi,+ chifukwa zimenezi n’zachilendo mu Isiraeli.+ Usachite chinthu chopusa, chochititsa manyazi ngati chimenechi.+

  • Ezekieli 22:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Munthu wachita zinthu zonyansa ndi mkazi wa mnzake,+ ndipo munthu wachita khalidwe lotayirira mwa kugona ndi mkazi wa mwana wake.+ Munthu wagona ndi mlongo wake, mwana wamkazi wa bambo ake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena