Genesis 34:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako Sekemu anaona mtsikanayu. Sekemuyu anali mwana wamwamuna wa Hamori, Mhivi,+ mmodzi wa atsogoleri a m’dzikolo. Atamuona, anamutenga n’kumugwiririra.+
2 Kenako Sekemu anaona mtsikanayu. Sekemuyu anali mwana wamwamuna wa Hamori, Mhivi,+ mmodzi wa atsogoleri a m’dzikolo. Atamuona, anamutenga n’kumugwiririra.+