Ekisodo 20:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Usalakelake nyumba ya mnzako. Usalakelake mkazi wa mnzako,+ kapolo wake wamwamuna, kapolo wake wamkazi, ng’ombe yake, bulu wake, kapena chilichonse cha mnzako.”+ Levitiko 19:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “‘Musabe,+ musanamizane+ ndipo aliyense asachitire mnzake chinyengo.+ 1 Akorinto 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tsopano pa nkhani imene munalemba ija, ndi bwino kuti mwamuna asakhudze+ mkazi.
17 “Usalakelake nyumba ya mnzako. Usalakelake mkazi wa mnzako,+ kapolo wake wamwamuna, kapolo wake wamkazi, ng’ombe yake, bulu wake, kapena chilichonse cha mnzako.”+