Levitiko 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Munthu akachimwa mwa kuchita mosakhulupirika kwa Yehova+ chifukwa wanyenga+ mnzake pa chinthu chimene chili m’manja mwake, kapena chimene mnzake wam’sungitsa,+ kapena wafwamba mnzake, kapena wam’bera mwachinyengo,+ Miyambo 12:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Milomo yonama imam’nyansa Yehova,+ koma anthu ochita zinthu mokhulupirika amam’sangalatsa.+ Aefeso 4:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Chotero, popeza tsopano mwataya chinyengo,+ aliyense wa inu alankhule zoona kwa mnzake,+ chifukwa ndife ziwalo za thupi limodzi.+
2 “Munthu akachimwa mwa kuchita mosakhulupirika kwa Yehova+ chifukwa wanyenga+ mnzake pa chinthu chimene chili m’manja mwake, kapena chimene mnzake wam’sungitsa,+ kapena wafwamba mnzake, kapena wam’bera mwachinyengo,+
25 Chotero, popeza tsopano mwataya chinyengo,+ aliyense wa inu alankhule zoona kwa mnzake,+ chifukwa ndife ziwalo za thupi limodzi.+