1 Mafumu 13:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mneneri wokalambayo atamva zimenezi, anati: “Inenso ndine mneneri ngati iweyo. Mngelo+ wandiuza mawu ochokera kwa Yehova akuti, ‘Kam’bweze upite naye kunyumba kwako kuti akadye chakudya ndi kumwa madzi.’” (Anamunamiza.)+ Yeremiya 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Aliyense amapusitsa mnzake+ ndipo salankhula choonadi ngakhale pang’ono. Aphunzitsa lilime lawo kulankhula chinyengo.+ Iwo adzitopetsa okha ndi kuchita zinthu zoipa.+
18 Mneneri wokalambayo atamva zimenezi, anati: “Inenso ndine mneneri ngati iweyo. Mngelo+ wandiuza mawu ochokera kwa Yehova akuti, ‘Kam’bweze upite naye kunyumba kwako kuti akadye chakudya ndi kumwa madzi.’” (Anamunamiza.)+
5 Aliyense amapusitsa mnzake+ ndipo salankhula choonadi ngakhale pang’ono. Aphunzitsa lilime lawo kulankhula chinyengo.+ Iwo adzitopetsa okha ndi kuchita zinthu zoipa.+