Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 22:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Koma mngelo wa Yehovayo anauza Balamu kuti: “Pita nawo limodzi anthuwa,+ koma ukanene zokhazo zimene ndikuuze.”+ Choncho Balamu anapitiriza ulendo wake limodzi ndi akalonga a Balakiwo.

  • Oweruza 6:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Kenako, kunabwera mngelo wa Yehova+ ndi kukhala pansi pa mtengo waukulu umene unali ku Ofira. Mtengo umenewu unali wa Yowasi, Mwabi-ezeri.+ Pa nthawiyi, Gidiyoni+ mwana wa Yowasi, anali kupuntha tirigu moponderamo mphesa kuti akamubise mwamsanga Amidiyani asanaone.

  • Agalatiya 1:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Komabe, ngati ifeyo kapena mngelo wochokera kumwamba angalengeze nkhani ina kwa inu monga uthenga wabwino, koma nkhaniyo n’kukhala yosiyana ndi uthenga wabwino umene tinaulengeza kwa inu, ameneyo akhale wotembereredwa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena