1 Akorinto 16:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ngati wina aliyense sakonda Ambuye, atembereredwe.+ Inde, idzani Ambuye!+ Agalatiya 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndikanakonda kuti anthu amene akufuna kukupotozani maganizo,+ afulidwe.+