Genesis 49:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma uta wake unakhalabe pamalo ake achikhalire,+ ndipo manja ake anali amphamvu ndi ochenjera.+ M’busayo, Mwala wa Isiraeli,+ akuchokera m’manja mwa Wamphamvu wa Yakobo.+ M’busayo akuchokera kumeneko ndithu. Aheberi 11:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Nanga ndinenenso chiyani pamenepa? Nthawi indichepera kuti ndipitirize kufotokoza za Gidiyoni,+ Baraki,+ Samisoni,+ Yefita,+ Davide,+ komanso Samueli+ ndi aneneri enanso.+
24 Koma uta wake unakhalabe pamalo ake achikhalire,+ ndipo manja ake anali amphamvu ndi ochenjera.+ M’busayo, Mwala wa Isiraeli,+ akuchokera m’manja mwa Wamphamvu wa Yakobo.+ M’busayo akuchokera kumeneko ndithu.
32 Nanga ndinenenso chiyani pamenepa? Nthawi indichepera kuti ndipitirize kufotokoza za Gidiyoni,+ Baraki,+ Samisoni,+ Yefita,+ Davide,+ komanso Samueli+ ndi aneneri enanso.+