Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 13:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Wa fuko la Efuraimu anali Hoshiya,+ mwana wa Nuni.

  • Yoswa 1:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ukhale wolimba mtima ndipo uchite zinthu mwamphamvu,+ pakuti ndiwe amene utsogolere anthuwa kuti akalandire dziko+ limene ndinalumbirira makolo awo kuti ndidzawapatsa.+

  • Yoswa 8:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Tsopano Yehova anauza Yoswa kuti: “Lozetsa nthungo* imene ili m’dzanja lako ku Ai,+ pakuti mzindawo ndaupereka m’manja mwako.”+ Chotero Yoswa analozetsa kumzindawo nthungo imene inali m’dzanja lake.

  • Oweruza 6:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Atatero, Yehova anamuyang’ana ndi kunena kuti: “Pita ndi mphamvu zimene ndakupatsazi,+ ndipo udzapulumutsadi Isiraeli m’manja mwa Amidiyani.+ Si ine amene ndakutuma kodi?”+

  • Oweruza 11:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Zitatero Yefita anapita kwa ana a Amoni kukamenyana nawo ndipo Yehova anawapereka m’manja mwake.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena