Genesis 45:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho Mulungu ananditumiza kuno patsogolo panu, kuti pakhale otsalira a anthu inu padziko lapansi,+ ndi kuti mukhalebe ndi moyo mwa chipulumutso chachikulu. Genesis 50:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Inu munali ndi cholinga chondichitira zoipa. Koma Mulungu anali ndi cholinga chabwino, kuti apulumutse miyoyo ya anthu ambiri ngati mmene akuchitira panomu.+ Yesaya 28:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Chotero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ndikuika mwala mu Ziyoni+ kuti ukhale maziko. Umenewu ndi mwala+ wapakona woyesedwa,+ wamtengo wapatali,+ woti ukhale maziko olimba.+ Palibe munthu woukhulupirira amene adzade nkhawa.+ Mateyu 21:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Ndiyeno Yesu anawafunsa kuti: “Kodi simunawerenge zimene Malemba amanena zakuti, ‘Mwala umene omanga nyumba anaukana+ ndi umene wakhala mwala wapakona wofunika kwambiri.+ Umenewu wachokera kwa Yehova, ndipo ndi wodabwitsa m’maso mwathu’? 1 Petulo 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamene mukubwera kwa iye, amene ndiye mwala wamoyo+ umene anthu+ anaukana,+ koma umene Mulungu anausankha, umenenso uli wamtengo wapatali kwa iye,+
7 Choncho Mulungu ananditumiza kuno patsogolo panu, kuti pakhale otsalira a anthu inu padziko lapansi,+ ndi kuti mukhalebe ndi moyo mwa chipulumutso chachikulu.
20 Inu munali ndi cholinga chondichitira zoipa. Koma Mulungu anali ndi cholinga chabwino, kuti apulumutse miyoyo ya anthu ambiri ngati mmene akuchitira panomu.+
16 Chotero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ndikuika mwala mu Ziyoni+ kuti ukhale maziko. Umenewu ndi mwala+ wapakona woyesedwa,+ wamtengo wapatali,+ woti ukhale maziko olimba.+ Palibe munthu woukhulupirira amene adzade nkhawa.+
42 Ndiyeno Yesu anawafunsa kuti: “Kodi simunawerenge zimene Malemba amanena zakuti, ‘Mwala umene omanga nyumba anaukana+ ndi umene wakhala mwala wapakona wofunika kwambiri.+ Umenewu wachokera kwa Yehova, ndipo ndi wodabwitsa m’maso mwathu’?
4 Pamene mukubwera kwa iye, amene ndiye mwala wamoyo+ umene anthu+ anaukana,+ koma umene Mulungu anausankha, umenenso uli wamtengo wapatali kwa iye,+