Genesis 45:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma Mulungu ananditumiza kuno, kuti anthu inu musatheretu+ padziko lapansi,* komanso kuti mukhalebe ndi moyo pokupulumutsani modabwitsa.
7 Koma Mulungu ananditumiza kuno, kuti anthu inu musatheretu+ padziko lapansi,* komanso kuti mukhalebe ndi moyo pokupulumutsani modabwitsa.