Genesis 45:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho Mulungu ananditumiza kuno patsogolo panu, kuti pakhale otsalira a anthu inu padziko lapansi,+ ndi kuti mukhalebe ndi moyo mwa chipulumutso chachikulu.
7 Choncho Mulungu ananditumiza kuno patsogolo panu, kuti pakhale otsalira a anthu inu padziko lapansi,+ ndi kuti mukhalebe ndi moyo mwa chipulumutso chachikulu.