Yesaya 51:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndidzaika mawu anga m’kamwa mwako+ ndipo ndidzakuphimba ndi mthunzi wa dzanja langa.+ Ndidzachita zimenezi n’cholinga choti ndikhazikitse kumwamba+ ndi kuyala maziko a dziko lapansi,+ ndiponso kuti ndiuze Ziyoni kuti, ‘Ndinu anthu anga.’+ Mateyu 16:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Chotero inenso ndikukuuza kuti, Iwe ndiwe Petulo,+ ndipo pathanthwe+ ili ndidzamangapo mpingo wanga. Zipata za Manda+ sizidzaugonjetsa.+ 1 Akorinto 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti palibe munthu wina amene angayale maziko ena+ alionse kupatulapo amene anayalidwawo, omwe ndi Yesu Khristu.+ Aefeso 2:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mwamangidwa pamaziko+ a atumwi+ ndi aneneri,+ ndipo Khristu Yesuyo ndiye mwala wapakona wa mazikowo.+
16 Ndidzaika mawu anga m’kamwa mwako+ ndipo ndidzakuphimba ndi mthunzi wa dzanja langa.+ Ndidzachita zimenezi n’cholinga choti ndikhazikitse kumwamba+ ndi kuyala maziko a dziko lapansi,+ ndiponso kuti ndiuze Ziyoni kuti, ‘Ndinu anthu anga.’+
18 Chotero inenso ndikukuuza kuti, Iwe ndiwe Petulo,+ ndipo pathanthwe+ ili ndidzamangapo mpingo wanga. Zipata za Manda+ sizidzaugonjetsa.+
11 Pakuti palibe munthu wina amene angayale maziko ena+ alionse kupatulapo amene anayalidwawo, omwe ndi Yesu Khristu.+
20 Mwamangidwa pamaziko+ a atumwi+ ndi aneneri,+ ndipo Khristu Yesuyo ndiye mwala wapakona wa mazikowo.+