Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 66:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Ndani anamvapo zinthu ngati zimenezi?+ Ndani anaonapo zinthu zoterezi?+ Kodi dziko+ limatulutsidwa ndi zowawa za pobereka tsiku limodzi lokha?+ Kapena kodi mtundu+ umabadwa nthawi imodzi?+ Pakuti Ziyoni wamva zowawa za pobereka ndipo wabereka ana ake aamuna.

  • Yesaya 66:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 “Pakuti monga momwe kumwamba kwatsopano+ ndi dziko lapansi latsopano+ zimene ndikupanga zidzakhalirebe pamaso panga,+ momwemonso ana anu+ ndi dzina lanu zidzakhalapo mpaka kalekale,”+ akutero Yehova.

  • Chivumbulutso 21:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Tsopano ndinaona kumwamba+ kwatsopano ndi dziko lapansi+ latsopano, pakuti kumwamba+ kwakale ndi dziko lapansi lakale+ zinali zitachoka, ndipo kulibenso nyanja.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena