Yesaya 54:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Kwa kanthawi kochepa ndinakusiyiratu,+ koma ndidzakusonkhanitsa pamodzi mwachifundo chachikulu.+ Yeremiya 30:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ana ake aamuna adzabwerera mwakale ndipo khamu la anthu ake lidzakhazikika pamaso panga.+ Ndidzalanga onse omupondereza.+
20 Ana ake aamuna adzabwerera mwakale ndipo khamu la anthu ake lidzakhazikika pamaso panga.+ Ndidzalanga onse omupondereza.+