Salimo 102:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ana a atumiki anu adzapitiriza kukhala motetezeka pamaso panu.+Ndipo ana awo adzakhazikika pamaso panu.”+ Yesaya 1:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndidzakubweretseraninso oweruza ngati pa chiyambi paja, ndi aphungu ngati poyamba paja.+ Pambuyo pa zimenezi mudzatchedwa Mzinda Wachilungamo ndi Mzinda Wokhulupirika.+
28 Ana a atumiki anu adzapitiriza kukhala motetezeka pamaso panu.+Ndipo ana awo adzakhazikika pamaso panu.”+
26 Ndidzakubweretseraninso oweruza ngati pa chiyambi paja, ndi aphungu ngati poyamba paja.+ Pambuyo pa zimenezi mudzatchedwa Mzinda Wachilungamo ndi Mzinda Wokhulupirika.+