2 Samueli 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Masiku ako akadzakwana,+ ndipo ukadzagona pamodzi ndi makolo ako,+ pamenepo ndidzautsa mbewu yako yobwera pambuyo pako, imene idzatuluka m’chiuno mwako. Ndipo ndidzakhazikitsadi ufumu wake.+ Salimo 90:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ntchito zanu zionekere kwa atumiki anu,+Ndipo ulemerero wanu uonekere pa ana awo.+ Yesaya 66:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Pakuti monga momwe kumwamba kwatsopano+ ndi dziko lapansi latsopano+ zimene ndikupanga zidzakhalirebe pamaso panga,+ momwemonso ana anu+ ndi dzina lanu zidzakhalapo mpaka kalekale,”+ akutero Yehova.
12 Masiku ako akadzakwana,+ ndipo ukadzagona pamodzi ndi makolo ako,+ pamenepo ndidzautsa mbewu yako yobwera pambuyo pako, imene idzatuluka m’chiuno mwako. Ndipo ndidzakhazikitsadi ufumu wake.+
22 “Pakuti monga momwe kumwamba kwatsopano+ ndi dziko lapansi latsopano+ zimene ndikupanga zidzakhalirebe pamaso panga,+ momwemonso ana anu+ ndi dzina lanu zidzakhalapo mpaka kalekale,”+ akutero Yehova.