Yesaya 65:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma kondwerani anthu inu,+ ndipo sangalalani kwamuyaya ndi zimene ndikulenga.+ Pakuti ndikulenga Yerusalemu kuti akhale chinthu chosangalatsa ndipo anthu ake akhale chinthu chokondweretsa.+
18 Koma kondwerani anthu inu,+ ndipo sangalalani kwamuyaya ndi zimene ndikulenga.+ Pakuti ndikulenga Yerusalemu kuti akhale chinthu chosangalatsa ndipo anthu ake akhale chinthu chokondweretsa.+