Salimo 67:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inu Mulungu, mitundu ya anthu ikutamandeni,+Ndithu mitundu yonse ya anthu ikutamandeni.+