Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezara 3:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Kenako Yesuwa+ mwana wa Yehozadaki ndi abale ake ansembe, ndiponso Zerubabele+ mwana wa Salatiyeli+ ndi abale ake, ananyamuka n’kumanga guwa lansembe la Mulungu wa Isiraeli kuti aziperekerapo nsembe zopsereza, mogwirizana ndi zimene zinalembedwa+ m’chilamulo cha Mose munthu wa Mulungu woona.

  • Ezara 5:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Panali pa nthawi imeneyi pamene Zerubabele+ mwana wa Salatiyeli+ ndi Yesuwa+ mwana wa Yehozadaki ananyamuka n’kuyamba kumanganso nyumba ya Mulungu. Nyumbayi inali ku Yerusalemu ndipo panali aneneri a Mulungu+ omwe anali kuwathandiza.

  • Yesaya 65:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 “Pakuti ndikulenga kumwamba kwatsopano+ ndi dziko lapansi latsopano.+ Zinthu zakale sizidzakumbukiridwanso+ ndipo sizidzabweranso mumtima.+

  • 2 Petulo 3:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Koma pali kumwamba kwatsopano+ ndi dziko lapansi latsopano+ zimene ife tikuyembekezera mogwirizana ndi lonjezo lake, ndipo mmenemo mudzakhala chilungamo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena