Ezara 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koresi mfumu ya Perisiya anatuma msungichuma Mitiredati yemwe anabweretsa ziwiyazo n’kuziwerenga. Atatero anazipereka kwa Sezibazara*+ mtsogoleri wa Yuda.+ Hagai 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Uza Zerubabele bwanamkubwa wa Yuda kuti,+ ‘Ine ndigwedeza kumwamba ndi dziko lapansi.+ Luka 3:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 mwana wa Yoanani,mwana wa Resa,mwana wa Zerubabele,+mwana wa Salatiyeli,+mwana wa Neri,
8 Koresi mfumu ya Perisiya anatuma msungichuma Mitiredati yemwe anabweretsa ziwiyazo n’kuziwerenga. Atatero anazipereka kwa Sezibazara*+ mtsogoleri wa Yuda.+