Ezara 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pa nthawi imeneyi ndi pamene Zerubabele+ mwana wa Salatiyeli ndi Yesuwa+ mwana wa Yehozadaki anayamba kumanganso nyumba ya Mulungu+ yomwe inali ku Yerusalemu. Aneneri a Mulungu anali nawo limodzi ndipo ankawathandiza.+ Ezara Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:2 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),3/2022, ptsa. 17-18
2 Pa nthawi imeneyi ndi pamene Zerubabele+ mwana wa Salatiyeli ndi Yesuwa+ mwana wa Yehozadaki anayamba kumanganso nyumba ya Mulungu+ yomwe inali ku Yerusalemu. Aneneri a Mulungu anali nawo limodzi ndipo ankawathandiza.+