Ekisodo 20:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mundipangire guwa lansembe ladothi,+ ndipo muziperekapo nsembe zanu zopsereza ndi nsembe zachiyanjano,* nkhosa zanu ndi ng’ombe zanu.+ M’malo onse amene ndidzachititsa dzina langa kukumbukika ndidzabwera kwa inu ndipo ndidzakudalitsani ndithu.+ Ekisodo 40:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndiyeno anaika guwa lansembe+ zopsereza pakhomo la chihema chopatulika, kapena kuti chihema chokumanako, kuti aziperekerapo nsembe yopsereza+ ndi nsembe yambewu, monga mmene Yehova analamulira Mose.
24 Mundipangire guwa lansembe ladothi,+ ndipo muziperekapo nsembe zanu zopsereza ndi nsembe zachiyanjano,* nkhosa zanu ndi ng’ombe zanu.+ M’malo onse amene ndidzachititsa dzina langa kukumbukika ndidzabwera kwa inu ndipo ndidzakudalitsani ndithu.+
29 Ndiyeno anaika guwa lansembe+ zopsereza pakhomo la chihema chopatulika, kapena kuti chihema chokumanako, kuti aziperekerapo nsembe yopsereza+ ndi nsembe yambewu, monga mmene Yehova analamulira Mose.