Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 6:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “Lamula Aroni ndi ana ake kuti, ‘Lamulo la nsembe yopsereza+ lili motere: Nsembe yopsereza izikhala pamoto, paguwa lansembe, usiku wonse kufikira m’mawa, ndipo moto wa paguwapo uzisonkhezeredwa.

  • Yobu 1:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Akamaliza kuchita maphwando kunyumba zawo zonse, Yobu anali kutumiza uthenga n’kuwauza kuti adziyeretse.+ Kenako iye anali kudzuka m’mawa kwambiri n’kupereka nsembe zopsereza+ mogwirizana ndi chiwerengero cha ana ake onse, popeza iye ankati, “mwina ana anga achimwa ndipo anyoza+ Mulungu mumtima mwawo.”+ Umu ndi mmene Yobu anali kuchitira nthawi zonse.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena