-
Yobu 1:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Akamaliza kuchita maphwando kunyumba zawo zonse, Yobu ankawaitana kuti adzawayeretse. Kenako iye ankadzuka mʼmamawa kwambiri nʼkuperekera mwana aliyense nsembe zopsereza.+ Chifukwa iye ankati: “Mwina ana anga achimwa ndipo anyoza Mulungu mumtima mwawo.” Izi ndi zimene Yobu ankachita nthawi zonse.+
-