Levitiko 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Lamula Aroni ndi ana ake kuti, ‘Ili ndi lamulo la nsembe yopsereza:+ Nsembe yopsereza izikhala pamoto, paguwa lansembe, usiku wonse mpaka mʼmawa ndipo moto wapaguwapo uzikhala ukuyaka nthawi zonse.
9 “Lamula Aroni ndi ana ake kuti, ‘Ili ndi lamulo la nsembe yopsereza:+ Nsembe yopsereza izikhala pamoto, paguwa lansembe, usiku wonse mpaka mʼmawa ndipo moto wapaguwapo uzikhala ukuyaka nthawi zonse.