Levitiko 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Lamula Aroni ndi ana ake kuti, ‘Lamulo la nsembe yopsereza+ lili motere: Nsembe yopsereza izikhala pamoto, paguwa lansembe, usiku wonse kufikira m’mawa, ndipo moto wa paguwapo uzisonkhezeredwa.
9 “Lamula Aroni ndi ana ake kuti, ‘Lamulo la nsembe yopsereza+ lili motere: Nsembe yopsereza izikhala pamoto, paguwa lansembe, usiku wonse kufikira m’mawa, ndipo moto wa paguwapo uzisonkhezeredwa.