2 Mafumu 5:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pamapeto pake, Namani anati: “Ngati mukukana, chonde ine mtumiki wanu, mundipatseko dothi+ lotha kunyamulidwa ndi nyulu* ziwiri, chifukwa sindidzaperekanso nsembe yopsereza kapena nsembe ina iliyonse kwa milungu ina, koma kwa Yehova basi.+
17 Pamapeto pake, Namani anati: “Ngati mukukana, chonde ine mtumiki wanu, mundipatseko dothi+ lotha kunyamulidwa ndi nyulu* ziwiri, chifukwa sindidzaperekanso nsembe yopsereza kapena nsembe ina iliyonse kwa milungu ina, koma kwa Yehova basi.+