Yesaya 64:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kuyambira kalekale palibe amene anamvapo+ kapena kuganizira za Mulungu wina kupatula inu,+ ndipo palibe amene anamuonapo. Inu mumathandiza munthu amene akukuyembekezerani.+
4 Kuyambira kalekale palibe amene anamvapo+ kapena kuganizira za Mulungu wina kupatula inu,+ ndipo palibe amene anamuonapo. Inu mumathandiza munthu amene akukuyembekezerani.+