Salimo 118:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mwala umene omanga nyumba anaukana+Wakhala mwala wofunika kwambiri wapakona.+ Mateyu 21:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Ndiyeno Yesu anawafunsa kuti: “Kodi simunawerenge zimene Malemba amanena zakuti, ‘Mwala umene omanga nyumba anaukana+ ndi umene wakhala mwala wapakona wofunika kwambiri.+ Umenewu wachokera kwa Yehova, ndipo ndi wodabwitsa m’maso mwathu’? Machitidwe 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yesu ameneyu ndiye ‘mwala umene inu omanga nyumba munauona ngati wopanda pake, umene tsopano wakhala mwala wofunika kwambiri wapakona.’+ Aefeso 2:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mwamangidwa pamaziko+ a atumwi+ ndi aneneri,+ ndipo Khristu Yesuyo ndiye mwala wapakona wa mazikowo.+
42 Ndiyeno Yesu anawafunsa kuti: “Kodi simunawerenge zimene Malemba amanena zakuti, ‘Mwala umene omanga nyumba anaukana+ ndi umene wakhala mwala wapakona wofunika kwambiri.+ Umenewu wachokera kwa Yehova, ndipo ndi wodabwitsa m’maso mwathu’?
11 Yesu ameneyu ndiye ‘mwala umene inu omanga nyumba munauona ngati wopanda pake, umene tsopano wakhala mwala wofunika kwambiri wapakona.’+
20 Mwamangidwa pamaziko+ a atumwi+ ndi aneneri,+ ndipo Khristu Yesuyo ndiye mwala wapakona wa mazikowo.+