Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 53:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Iye ananyozedwa ndipo anthu anali kumupewa.+ Anali munthu amene anadziwa kupweteka ndiponso amene anadziwa matenda.+ Ife tinali kuyang’ana kumbali kuti tisaone nkhope yake.+ Ananyozedwa ndipo tinamuona ngati wopanda pake.+

  • Maliko 12:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Kodi simunawerengepo lemba limene limati, ‘Mwala+ umene omanga nyumba anaukana, umenewu wakhala mwala wapakona wofunika kwambiri’?+

  • Luka 20:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Koma iye anawayang’ana ndi kunena kuti: “Pajatu malemba amati, ‘Mwala umene omanga nyumba anaukana,+ umenewu wakhala mwala wapakona wofunika kwambiri.’+ Kodi mawu amenewa amatanthauza chiyani?

  • 1 Petulo 2:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Pamene mukubwera kwa iye, amene ndiye mwala wamoyo+ umene anthu+ anaukana,+ koma umene Mulungu anausankha, umenenso uli wamtengo wapatali kwa iye,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena