Salimo 118:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mwala umene omanga nyumba anaukana+Wakhala mwala wofunika kwambiri wapakona.+ 1 Petulo 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho iye ndi wamtengo wapatali kwa inu chifukwa ndinu okhulupirira, koma kwa osakhulupirira, “mwala umene omanga nyumba anaukana,+ umenewu wakhala mwala wapakona wofunika kwambiri,”+
7 Choncho iye ndi wamtengo wapatali kwa inu chifukwa ndinu okhulupirira, koma kwa osakhulupirira, “mwala umene omanga nyumba anaukana,+ umenewu wakhala mwala wapakona wofunika kwambiri,”+