Deuteronomo 33:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Mulungu wakale lomwe ndiwo malo ako obisalamo,+Ndipo iwe uli m’manja amene adzakhalapo mpaka kalekale.+Adzapitikitsa mdani pamaso pako,+Ndipo adzanena kuti, ‘Awononge!’+ Salimo 91:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 91 Aliyense wokhala m’malo otetezeka+ a Wam’mwambamwamba+Adzakhala wosungika mumthunzi wa Wamphamvuyonse.+ Yesaya 49:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye anachititsa m’kamwa mwanga kukhala ngati lupanga lakuthwa.+ Anandibisa mumthunzi+ wa dzanja lake.+ Anandisandutsa muvi wonola bwino. Anandibisa m’kachikwama kake koikamo mivi.
27 Mulungu wakale lomwe ndiwo malo ako obisalamo,+Ndipo iwe uli m’manja amene adzakhalapo mpaka kalekale.+Adzapitikitsa mdani pamaso pako,+Ndipo adzanena kuti, ‘Awononge!’+
91 Aliyense wokhala m’malo otetezeka+ a Wam’mwambamwamba+Adzakhala wosungika mumthunzi wa Wamphamvuyonse.+
2 Iye anachititsa m’kamwa mwanga kukhala ngati lupanga lakuthwa.+ Anandibisa mumthunzi+ wa dzanja lake.+ Anandisandutsa muvi wonola bwino. Anandibisa m’kachikwama kake koikamo mivi.