Salimo 46:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova wa makamu ali ndi ife.+Mulungu wa Yakobo ndiye malo athu okwezeka ndiponso achitetezo.+ [Seʹlah.] Salimo 90:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 90 Inu Yehova, ndinudi malo athu okhalamo+Ku mibadwomibadwo.+ Salimo 91:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndidzauza Yehova kuti: “Inu ndinu pothawirapo panga ndi malo anga achitetezo,+Mulungu wanga amene ndimamukhulupirira.”+ Salimo 125:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova wazungulira anthu ake+Ngati mmene mapiri azungulirira Yerusalemu,+Kuyambira tsopano mpaka kalekale.+
11 Yehova wa makamu ali ndi ife.+Mulungu wa Yakobo ndiye malo athu okwezeka ndiponso achitetezo.+ [Seʹlah.]
2 Ndidzauza Yehova kuti: “Inu ndinu pothawirapo panga ndi malo anga achitetezo,+Mulungu wanga amene ndimamukhulupirira.”+
2 Yehova wazungulira anthu ake+Ngati mmene mapiri azungulirira Yerusalemu,+Kuyambira tsopano mpaka kalekale.+