Yesaya 28:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ndikuika mwala woyesedwa mu Ziyoni kuti ukhale maziko,+Umenewu ndi mwala wapakona wamtengo wapatali+ wa maziko olimba.+ Palibe munthu woukhulupirira amene adzade nkhawa.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 28:16 Yesaya 1, ptsa. 293-294 Nsanja ya Olonda,6/1/1991, tsa. 17
16 Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ndikuika mwala woyesedwa mu Ziyoni kuti ukhale maziko,+Umenewu ndi mwala wapakona wamtengo wapatali+ wa maziko olimba.+ Palibe munthu woukhulupirira amene adzade nkhawa.+