Genesis 37:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iwo anamuonera patali akubwera, ndipo asanafike pafupi anayamba kupangana chiwembu choti amuphe.+ Genesis 45:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma musadzimvere chisoni+ kapena kudzipsera mtima kuti munandigulitsa kuno. Mulungu ndiye ananditumiza patsogolo panu kuti ndidzapulumutse miyoyo yanu.+ Salimo 105:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mulungu anatsogoza munthu kuti anthu akewo abwere pambuyo pake,Anatumiza Yosefe amene anagulitsidwa kuti akhale kapolo.+ Salimo 119:71 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 71 Zili bwino kuti ndasautsika,+Kuti ndiphunzire malamulo anu.+ Aroma 8:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Tikudziwa tsopano kuti Mulungu amagwirizanitsa zochita zake zonse+ pofuna kupindulitsa amene amakonda Mulungu, anthu oitanidwa mogwirizana ndi cholinga chake.+
5 Koma musadzimvere chisoni+ kapena kudzipsera mtima kuti munandigulitsa kuno. Mulungu ndiye ananditumiza patsogolo panu kuti ndidzapulumutse miyoyo yanu.+
17 Mulungu anatsogoza munthu kuti anthu akewo abwere pambuyo pake,Anatumiza Yosefe amene anagulitsidwa kuti akhale kapolo.+
28 Tikudziwa tsopano kuti Mulungu amagwirizanitsa zochita zake zonse+ pofuna kupindulitsa amene amakonda Mulungu, anthu oitanidwa mogwirizana ndi cholinga chake.+