Salimo 37:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Oipa asolola lupanga ndipo akunga uta wawo,+Kuti agwetse osautsika ndi osauka,+Kuti aphe anthu amene njira zawo ndi zowongoka.+ Salimo 94:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iwo amaukira koopsa munthu wolungama,+Ndipo munthu wosalakwa amamuweruza kuti ndi woipa. Amachita zimenezi kuti akhetse magazi ake.+ Miyambo 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Maso odzikweza,+ lilime lonama,+ manja okhetsa magazi a anthu osalakwa,+ Mateyu 15:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mwachitsanzo, maganizo oipa, za kupha anthu, za chigololo, za dama, za kuba, maumboni onama, ndi zonyoza Mulungu,+ zimachokera mumtima.+
14 Oipa asolola lupanga ndipo akunga uta wawo,+Kuti agwetse osautsika ndi osauka,+Kuti aphe anthu amene njira zawo ndi zowongoka.+
21 Iwo amaukira koopsa munthu wolungama,+Ndipo munthu wosalakwa amamuweruza kuti ndi woipa. Amachita zimenezi kuti akhetse magazi ake.+
19 Mwachitsanzo, maganizo oipa, za kupha anthu, za chigololo, za dama, za kuba, maumboni onama, ndi zonyoza Mulungu,+ zimachokera mumtima.+