Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 23:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “Utalikirane ndi mawu onama.+ Usaphe munthu wosalakwa ndi munthu wolungama, chifukwa woipa sindidzamuyesa wolungama.+

  • 1 Mafumu 21:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Ukamuuze kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Kodi wapha munthu+ n’kutenganso munda wake?”’+ Ukamuuzenso kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Pamalo+ amene agalu ananyambita magazi a Naboti, pomweponso agalu adzanyambita magazi ako, a iweyo.”’”+

  • Miyambo 17:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Aliyense wonena kuti munthu woipa ndi wolungama+ ndiponso aliyense wonena kuti munthu wolungama ndi woipa,+ onsewa ndi onyansa kwa Yehova.+

  • Machitidwe 7:58
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 58 Atamutulutsira kunja kwa mzinda,+ anayamba kumuponya miyala.+ Ndipo mboni+ zinaika malaya awo akunja pafupi ndi mnyamata wina dzina lake Saulo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena