Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 21:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Kenako amuna awiri opanda pake anabwera n’kukhala patsogolo pa Naboti. Ndiyeno amuna opanda pakewo anayamba kupereka umboni wotsutsana ndi Naboti pamaso pa anthuwo, wakuti: “Naboti watemberera Mulungu ndi mfumu!”+ Pambuyo pake anamutulutsira kunja kwa mzindawo n’kumuponya miyala mpaka anafa.+

  • Luka 23:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Koma khamu lonse linafuulira pamodzi kuti: “Ameneyu muthane naye basi,+ koma ife mutimasulire Baraba!”+

  • Yakobo 5:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Mwaweruza ndi kupha munthu wolungama. Iye akukutsutsani.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena