Machitidwe 7:58 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 58 Kenako anamutulutsira kunja kwa mzinda nʼkuyamba kumuponya miyala.+ Ndipo mboni+ zinaika malaya awo akunja pafupi ndi mnyamata wina dzina lake Saulo.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:58 Nsanja ya Olonda,5/15/1999, tsa. 29
58 Kenako anamutulutsira kunja kwa mzinda nʼkuyamba kumuponya miyala.+ Ndipo mboni+ zinaika malaya awo akunja pafupi ndi mnyamata wina dzina lake Saulo.+