Ekisodo 21:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ngati wina wamwalira, pamenepo uzipereka moyo kulipira moyo.+ Salimo 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iye wafukula dzenje, walikumbadi.+Koma adzagwera m’dzenje lokumba yekha.+