Aheberi 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Zinthu zonse zilipo kuti zipereke ulemerero kwa Mulungu ndipo zinakhalapo kudzera mwa iye.+ Choncho pamene akuika ana ambiri pa ulemerero,+ n’koyenera kuti achititse Mtumiki Wamkulu+ wa chipulumutso chawo kukhala wangwiro kudzera m’masautso.+ Aheberi 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndipo atakhala wangwiro,+ anakhala ndi udindo wopereka chipulumutso chamuyaya+ kwa onse omumvera,+
10 Zinthu zonse zilipo kuti zipereke ulemerero kwa Mulungu ndipo zinakhalapo kudzera mwa iye.+ Choncho pamene akuika ana ambiri pa ulemerero,+ n’koyenera kuti achititse Mtumiki Wamkulu+ wa chipulumutso chawo kukhala wangwiro kudzera m’masautso.+