Levitiko 8:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Musachoke pakhomo la chihema chokumanako kwa masiku 7,+ kufikira tsiku lomaliza la kulongedwa kwanu unsembe, chifukwa kukupatsani mphamvu* kudzatenga masiku 7.+ Aheberi 7:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Chilamulo chimaika amuna okhala ndi zofooka+ kukhala akulu a ansembe.+ Koma mawu a lumbiro+ amene ananenedwa pambuyo pa Chilamulo anaika Mwana, amene anakhala wangwiro+ kosatha.
33 Musachoke pakhomo la chihema chokumanako kwa masiku 7,+ kufikira tsiku lomaliza la kulongedwa kwanu unsembe, chifukwa kukupatsani mphamvu* kudzatenga masiku 7.+
28 Chilamulo chimaika amuna okhala ndi zofooka+ kukhala akulu a ansembe.+ Koma mawu a lumbiro+ amene ananenedwa pambuyo pa Chilamulo anaika Mwana, amene anakhala wangwiro+ kosatha.