Salimo 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndinene za lamulo la Yehova.Iye wandiuza kuti: “Iwe ndiwe mwana wanga,+Lero, ine ndakhala bambo ako.+ Salimo 110:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yehova walumbira+ (ndipo sadzasintha maganizo). Iye wati:+“Iwe ndiwe wansembe mpaka kalekale,+Monga mwa unsembe wa Melekizedeki!”+
7 Ndinene za lamulo la Yehova.Iye wandiuza kuti: “Iwe ndiwe mwana wanga,+Lero, ine ndakhala bambo ako.+
4 Yehova walumbira+ (ndipo sadzasintha maganizo). Iye wati:+“Iwe ndiwe wansembe mpaka kalekale,+Monga mwa unsembe wa Melekizedeki!”+