Ekisodo 29:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 “Uchite zimenezi kwa Aroni ndi ana ake malinga ndi zonse zimene ndakulamula.+ Udzatenga masiku 7 kuti uwapatse mphamvu. + Numeri 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Amenewa ndiwo anali mayina a ana a Aroni. Iwo anali ansembe odzozedwa amene anapatsidwa mphamvu* yotumikira monga ansembe.+
35 “Uchite zimenezi kwa Aroni ndi ana ake malinga ndi zonse zimene ndakulamula.+ Udzatenga masiku 7 kuti uwapatse mphamvu. +
3 Amenewa ndiwo anali mayina a ana a Aroni. Iwo anali ansembe odzozedwa amene anapatsidwa mphamvu* yotumikira monga ansembe.+