Levitiko 16:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Choncho Aroni azipereka ng’ombe yamphongo ya nsembe yake yamachimo, kuti aphimbe machimo ake ndi a nyumba yake. Akatero azipha ng’ombe ya nsembe yake yamachimoyo.+
11 “Choncho Aroni azipereka ng’ombe yamphongo ya nsembe yake yamachimo, kuti aphimbe machimo ake ndi a nyumba yake. Akatero azipha ng’ombe ya nsembe yake yamachimoyo.+