Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 19:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 “‘Musabe,+ musanamizane+ ndipo aliyense asachitire mnzake chinyengo.+

  • Deuteronomo 18:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 “‘Koma mneneri amene adzadzikuza mwa kulankhula m’dzina langa mawu amene sindinamulamule kuti alankhule,+ kapena kulankhula m’dzina la milungu ina,+ mneneri ameneyo afe ndithu.+

  • Yeremiya 29:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 “Anthu onse amene ali ku ukapolo uwatumizire uthenga+ wakuti, ‘Ponena za Semaya wa ku Nehelamu, Yehova wanena kuti: “Pakuti Semaya walosera kwa anthu inu, ngakhale kuti ine sindinamutume, ndipo wayesa kukuchititsani kukhulupirira zinthu zonama,+

  • Ezekieli 13:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Dzanja langa lalimbana ndi aneneri amene akuona masomphenya abodza ndiponso amene akulosera zonama.+ Iwo sadzapitiriza kukhala m’gulu la anthu anga apamtima,+ komanso sadzalembedwa m’buku la mayina a anthu a nyumba ya Isiraeli.+ Sadzabwera kudziko la Isiraeli+ ndipo anthu inu mudzadziwa kuti ine ndine Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa,+

  • Mateyu 7:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 “Chenjerani ndi aneneri onyenga+ amene amabwera kwa inu atavala ngati nkhosa,+ koma mkati mwawo ali mimbulu yolusa.+

  • 2 Petulo 2:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Komabe, pakati pa anthuwo panadzakhala aneneri onyenga. Momwemonso padzakhala aphunzitsi onyenga pakati panu.+ Amenewa adzabweretsa mwakachetechete timagulu tampatuko towononga ndipo adzakana ngakhale iye amene anawagula,+ n’kudzibweretsera chiwonongeko chofulumira.

  • 1 Yohane 4:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Okondedwa, musamakhulupirire mawu alionse ouziridwa,+ koma muziyesa mawu ouziridwawo kuti muone ngati ali ochokeradi kwa Mulungu,+ chifukwa aneneri onyenga ambiri alowa m’dziko.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena