Chivumbulutso 22:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako anandiuza kuti: “Mawu awa ndi odalirika ndiponso oona.+ Yehova, Mulungu wopereka mauthenga ouziridwa+ a aneneri,+ anatumiza mngelo wake kudzaonetsa akapolo ake zinthu zimene ziyenera kuchitika posachedwa.+
6 Kenako anandiuza kuti: “Mawu awa ndi odalirika ndiponso oona.+ Yehova, Mulungu wopereka mauthenga ouziridwa+ a aneneri,+ anatumiza mngelo wake kudzaonetsa akapolo ake zinthu zimene ziyenera kuchitika posachedwa.+